1 Mafumu 8:4 BL92

4 Ndipo anatenga likasa la Yehova, ndi cihema cokomanako, ndi zipangizo zonse zopatulika, zinali m'cihemamo, inde zimenezi anazitenga ansembe ndi Alevi.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 8

Onani 1 Mafumu 8:4 nkhani