16 Pakuti Farao mfumu ya Aigupto adakwera nalanda Gezeri, nautentha ndi moto, nawapha Akanani akukhala m'mudzimo, naupereka kwaulere kwa mwana wace mkazi wa Solomo.
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 9
Onani 1 Mafumu 9:16 nkhani