23 Ameneyo anali akulu a akapitao oyang'anira nchito ya Solomo, mazana asanu mphambu makumi asanu akulamulira anthu ogwira nchito aja.
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 9
Onani 1 Mafumu 9:23 nkhani