24 Koma mwana wamkazi wa Farao anaturuka m'mudzi wa Davide kukwera ku nyumba yace adammangira Solomo, pamenepo iye anamanganso Milo.
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 9
Onani 1 Mafumu 9:24 nkhani