Deuteronomo 24:17 BL92

17 Musamaipsa mlandu wa mlendo, kapena wa ana amasiye; kapena kutenga cikole cobvala ca mkazi wamasiye;

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 24

Onani Deuteronomo 24:17 nkhani