Deuteronomo 24:18 BL92

18 koma muzikumbukila kuti munali akapolo m'Aigupto, ndi kuti Yehova Mulungu wanu anakuombolaniko; cifukwa cace ndikuuzani kucita cinthu ici.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 24

Onani Deuteronomo 24:18 nkhani