Levitiko 10:14 BL92

14 Ndi nganga yoweyula ndi mwendo wokweza mudyere izi pamalo poyera; iwe ndi ana ako amuna, ndi ana ako akazi omwe, popeza zapatsidwa gawo lako ndi gawo la ana ako amuna, zocokera ku nsembe zoyamika za ana a Israyeli.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 10

Onani Levitiko 10:14 nkhani