Levitiko 11:26 BL92

26 Nyama iri yonse yakugawanika ciboda, koma yosagawanikitsa, ndi yosabzikula, muiyese yodetsa; ali yense wakuikhudza adzakhala wodetsedwa.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 11

Onani Levitiko 11:26 nkhani