Levitiko 11:37 BL92

37 Ndipo kanthu ka mtembo wace kakagwa pa mbeu yofesa, ikati ifesedwe, idzakhala yoyera.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 11

Onani Levitiko 11:37 nkhani