Levitiko 12:8 BL92

8 Ici ndi cilamulo ca kwa iye wakubala, kapena mwana wamwamuna kapena wamkazi. Ndipo cuma cace cikapanda kufikira nkhosa, atenge njiwa ziwiri kapena maunda awiri; lina likhale nsembe yopsereza, ndi lina nsembe yaucimo; ndi wansembe amcitire comtetezera, ndipo adzakhalawoyera.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 12

Onani Levitiko 12:8 nkhani