Levitiko 13:39 BL92

39 wansembe aziona; ndipo taonani ngati zikanga ziri pa khungu la thupi lao zikhala zotuwatuwa; ndilo thuza labuka pakhungu; ndiye woyera.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 13

Onani Levitiko 13:39 nkhani