Levitiko 14:11 BL92

11 Ndipo wansembe amene amyeretsayo, amuike munthu uja wakuti ayeretsedwe, ndi zinthu zija, pamaso pa Yehova, pa khomo la cihema cokomanako;

Werengani mutu wathunthu Levitiko 14

Onani Levitiko 14:11 nkhani