Levitiko 14:16 BL92

16 ndipo wansembe abviike cala cace ca dzanja lace lamanja ca iye mwini m'mafuta ali m'dzanja lace lamanzere, nawaze mafuta kasanu ndi kawiri ndi cala cace pamaso pa Yehova;

Werengani mutu wathunthu Levitiko 14

Onani Levitiko 14:16 nkhani