Levitiko 15:11 BL92

11 Ndipo munthu ali yense wakukhayo akamkhudza, osasambatu m'manja m'madzi, atsuke zobvala zace, nasambe m'madzi, nadzakhala wodetsedwa kufikira madzulo.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 15

Onani Levitiko 15:11 nkhani