15 ndipo wansembe azipereke izo, imodzi ikhale nsembe yaucimo, ndi yina nsembe yopsereza; ndipo wansembe amcitire comtetezera pamaso pa Yehova cifukwa ca kukha kwace.
Werengani mutu wathunthu Levitiko 15
Onani Levitiko 15:15 nkhani