Levitiko 15:2 BL92

2 Nenani nao ana a Israyeli, nimuti nao, Pamene mwamuna ali yense ali ndi nthenda yakukha m'thupi mwace, akhale wodetsedwa, cifukwaca kukha kwace.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 15

Onani Levitiko 15:2 nkhani