Levitiko 15:5 BL92

5 Ndipo munthu ali yense wakukhudza kama wace azitsuka zobvala zace, nasambe m'madzi, nadzakhala wodetsedwa kufikira madzulo,

Werengani mutu wathunthu Levitiko 15

Onani Levitiko 15:5 nkhani