Levitiko 16:10 BL92

10 Koma mbuzi imene adaigwera maere a Azazeli, aiike yamoyo pamaso pa Yehova, kuti acite nayo cotetezera, kuitumiza kucipululu ikhale ya Azazeli.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 16

Onani Levitiko 16:10 nkhani