Levitiko 16:19 BL92

19 Ndipo awazepo mwazi wina ndi cala cace kasanu ndi katatu; ndi kuliyeretsa ndi kulipatula kulicotsera zodetsa za ana a Israyeli.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 16

Onani Levitiko 16:19 nkhani