Levitiko 16:23 BL92

23 Pamenepo Aroni alowe m'cihema cokomanako, nabvule zobvala zabafuta zimene anazibvala polowa m'malo opatulika, nazisiye komweko.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 16

Onani Levitiko 16:23 nkhani