Levitiko 16:26 BL92

26 Ndipo iye amene anacotsa mbuzi ipite kwa Azazeli atsuke zobvala zace, nasambe thupi lace ndi madzi, ndipo atatero alowenso kucigono.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 16

Onani Levitiko 16:26 nkhani