Levitiko 16:3 BL92

3 Aroni azilowa pa bwalo la malo opatulika nazozo: ng'ombe yamphongo ikhale ya nsembe yaucimo, ndi nkhosa yamphongo ikhale ya nsembe yopsereza.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 16

Onani Levitiko 16:3 nkhani