Levitiko 17:13 BL92

13 Ndipo munthu ali yense wa ana a Israyeli, kapena mlendo wakugonera pakati pa inu, akasaka nyama kapena mbalame yakudya, nakaigwira; azikhetsa mwazi wace naufotsere ndi dothi.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 17

Onani Levitiko 17:13 nkhani