Levitiko 17:2 BL92

2 Nena ndi Aroni, ndi ana ace amuna, ndi ana a Israyeli onse, nuti nao, Ici ndi cimene Yehova wauza, ndi kuti,

Werengani mutu wathunthu Levitiko 17

Onani Levitiko 17:2 nkhani