Levitiko 18:24 BL92

24 Musamadzidetsa naco cimodzi ca izi; pakuti amitundu amene ndiwapitikitsa pamaso panu amadetsedwa nazo zonsezi;

Werengani mutu wathunthu Levitiko 18

Onani Levitiko 18:24 nkhani