Levitiko 18:3 BL92

3 Musamacita monga mwa macitidwe a dziko la Aigupto muja munakhalamo; musamacita monga mwa macitidwe a dziko la Kanani kumene ndipita nanuko, nimusamayenda m'malemba ao.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 18

Onani Levitiko 18:3 nkhani