Levitiko 18:5 BL92

5 Inde, muzisunga malemba anga, ndi maweruzo anga; amenewo munthu akawacita, adzakhala nao ndi moyo; Ine ndine Yehova.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 18

Onani Levitiko 18:5 nkhani