Levitiko 19:10 BL92

10 Usamakunkha khunkha la m'munda wako wamphesa, usamazitola zidagwazi za m'munda wako wamphesa; uzisiyire wosauka ndi mlendo; Ine ndine Yehova Mulungu wanu.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 19

Onani Levitiko 19:10 nkhani