Levitiko 19:13 BL92

13 Usamasautsa mnansi wako, kapena kulanda zace; mphotho yace ya wolipidwa isakhale ndi iwe kufikira m'mawa.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 19

Onani Levitiko 19:13 nkhani