Levitiko 19:20 BL92

20 Munthu akagona ndi mkazi, ndiye mdzakazi, wopalidwa ubwenzi ndi mwamuna, wosamuombola kapena wosapatsidwa ufulu, akwapulidwe; asawaphe, popeza si mfulu mkaziyo.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 19

Onani Levitiko 19:20 nkhani