29 Usamaipsa mwana wako wamkazi ndi kumcititsa cigololo; lingadzale ndi cigololo dzikoli, ndi kudzazidwa nazo zocititsa manyazi.
Werengani mutu wathunthu Levitiko 19
Onani Levitiko 19:29 nkhani