Levitiko 19:36 BL92

36 Mukhale naco coyesera coona, miyeso yoona, era woona, bini woona; Ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndinakuturutsani m'dziko la Aigupto.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 19

Onani Levitiko 19:36 nkhani