Levitiko 19:8 BL92

8 koma ali yense akudyako adzasenza mphulupulu yace, popeza waipsa copatulidwa ca Yehova; ndi munthuyo amsadze, kumcotsa kwa anthu a mtundu wace.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 19

Onani Levitiko 19:8 nkhani