Levitiko 2:16 BL92

16 Ndipo wansembe atenthe cikumbutso cace, atatapa pa tirigu wace wokonola, ndi pa mafuta ace, ndi kutenga libano lace lonse; ndiyo nsembe yamoto ya kwa Yehova.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 2

Onani Levitiko 2:16 nkhani