Levitiko 20:10 BL92

10 Munthu akacita cigololo ndi mkazi wa mwini, popeza wacita cigololo ndi mkazi wa mnansi wace, awaphe nditho, mwamuna ndi mkazi onse awiri.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 20

Onani Levitiko 20:10 nkhani