Levitiko 20:14 BL92

14 Munthu akatenga mkazi pamodzi ndi mai wace cocititsa manyazi ici; aziwatentha ndi moto, iye ndi iwowa; kuti pasakhale cocititsa manyazico pakati pa inu.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 20

Onani Levitiko 20:14 nkhani