Levitiko 21:12 BL92

12 Asaturuke m'malo opatulika, kapena kuipsa malo opatulika a Mulungu wace; popeza korona wa mafuta odzoza wa Mulungu wace ali pa iye; Ine ndine Yehova.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 21

Onani Levitiko 21:12 nkhani