Levitiko 21:14 BL92

14 Mkazi wamasiye, kapena womleka, kapena woipsidwa, wacigololo, oterewa asawatenge; koma azitenga namwali wa anthu a mtundu wace akhale mkazi wace.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 21

Onani Levitiko 21:14 nkhani