Levitiko 21:17 BL92

17 Nena ndi Aroni, kuti, Ali yense wa mbeu zako mwa mibadwo yao wakukhala naco cirema, asayandikize kupereka mkate wa Mulungu wace.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 21

Onani Levitiko 21:17 nkhani