Levitiko 21:21 BL92

21 Wa mbeu ya Aroni wansembe asayandikize mmodzi wokhala naco cirema, kupereka nsembe zamoto za Yehova; ali naco cirema asayandikize kupereka cakudya ca Mulungu wace.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 21

Onani Levitiko 21:21 nkhani