Levitiko 21:23 BL92

23 koma asafike ku nsaru yocinga, asayandikize ku guwa la nsembe, popeza ali naco cirema; kuti angaipse malo anga opatulika; popeza Ine ndine Yehova wakuwapatula.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 21

Onani Levitiko 21:23 nkhani