25 Ndipo musamazilandira izi ku dzanja la mlendo ndi kubwera nazo zikhale cakudya ca Mulungu wanu; popeza ziri nako kubvunda kwao; ziri ndi cirema; sizidzalandirikira inu.
Werengani mutu wathunthu Levitiko 22
Onani Levitiko 22:25 nkhani