6 munthu wokhudza ciri conse cotere adzakhala wodetsedwa kufikira madzulo, ndipo asadye zinthu zopatulika, akapanda kusamba thupi lace ndi madzi.
Werengani mutu wathunthu Levitiko 22
Onani Levitiko 22:6 nkhani