Levitiko 23:34 BL92

34 Nena ndi ana a Israyeli, kuti, Tsiku lakhumi ndi cisanu la mwezi uno wacisanu ndi ciwiri pali madyerero a misasa a Yehova, masiku asanu ndi awiri.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 23

Onani Levitiko 23:34 nkhani