Levitiko 23:41 BL92

41 Ndipo muwasunge madyerero a Yehova masiku asanu ndi awiri m'caka; ndilo lemba losatha mwa mibadwo yanu; musunge mwezi wacisanu ndi ciwiri.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 23

Onani Levitiko 23:41 nkhani