Levitiko 24:14 BL92

14 Turuka naye wotembererayo kunja kwa cigono; ndipo onse adamumva aike manja ao pamutu pace, ndi khamu lonse limponye miyala afe.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 24

Onani Levitiko 24:14 nkhani