Levitiko 24:16 BL92

16 Ndi iye wakucitira mwano dzina la Yehova, amuphe ndithu; khamu lonse limponye miyala ndithu; mlendo ndi wobadwa m'dziko yemwe akacitira dzina la Yehova mwano, awaphe.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 24

Onani Levitiko 24:16 nkhani