Levitiko 24:19 BL92

19 Munthu akacititsa mnansi wace cirema, monga umo anacitira momwemo amcitire iye;

Werengani mutu wathunthu Levitiko 24

Onani Levitiko 24:19 nkhani