Levitiko 24:5 BL92

5 Ndipo uzitenga ufa wosalala, ndi kuphika timitanda khumi ndi tiwiri; awiri a magawo khumi a efa afikane kamtanda kamodzi,

Werengani mutu wathunthu Levitiko 24

Onani Levitiko 24:5 nkhani