Levitiko 25:16 BL92

16 Monga mwa kucuruka kwa zaka zace uonjeze mtengo wace, ndi monga mwa kucepa kwa zaka zace ucepse mtengo wace; pakuti akugulitsa powerenga masiku ace.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 25

Onani Levitiko 25:16 nkhani